Ziŵelengelo Zonse za mu 2020
Nthambi za Mboni za Yehova: 87
Ciŵelengelo ca Maiko ocitila Lipoti: 240
Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 120,387
Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 17,844,773
Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 21,182
Ofalitsa Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikilaa: 8,695,808
Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,424,185
Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2019: -0.6
Onse Amene Anabatizikab: 241,994
Avaleji ya Apainiyac Mwezi Uliwonse: 1,299,619
Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 338,568
Maola Onse Amene Tinathela Mu Utumiki: 1,669,901,531
Avaleji ya Maphunzilo a Baibod Mwezi Uliwonse: 7,705,765
M’caka ca utumiki ca 2020,e Mboni za Yehova zinaseŵenzetsa ndalama zoposa madola 231 miliyoni posamalila apainiya apadela, amishonale komanso oyang’anila madela pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale na alongo okwana 20,994, amene akutumikila m’maofesi a nthambi. Onse amenewa ali m’Gulu la Padziko Lonse la Atumiki Apadela a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.
a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengelo cimeneci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.
b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.
c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.
d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?”
e Caka ca utumiki ca 2020 cinayamba pa September 1, 2019, ndipo cinasila pa August 31, 2020.