LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • syr23 tsa. 2
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2023

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2023
  • Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Nkhani Zofanana
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2022
    Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziwelengelo Zonse za mu 2024
    Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2024 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2021
    Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2019
    Lipoti la caka ca utumiki ca 2019 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
Onaninso Zina
Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
syr23 tsa. 2

Ziŵelengelo Zonse za mu 2023

  • Nthambi za Mboni za Yehova: 85

  • Ciŵelengelo ca Maiko Ocitila Lipoti: 239

  • Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 118,177

  • Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 20,461,767

  • Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 22,312

  • Ofalitsaa Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila: 8,816,562

  • Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali Kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,625,042

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2022: 1.3

  • Onse Amene Anabatizikab: 269,517

  • Avaleji ya Apainiyac Mwezi Uliwonse: 1,570,906

  • Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 738,457

  • Maola Onse Amene Tinathela mu Utumiki: 1,791,490,713

  • Avaleji ya Maphunzilo a Baibod Mwezi Uliwonse: 7,281,212

Caka ca utumiki ca 2023 cinayamba pa September 1, 2022, ndipo cinatha pa August 31, 2023.

a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengeloci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.

b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizike n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.

c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani