LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • syr21 tsa. 2
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2021

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2021
  • Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Nkhani Zofanana
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2022
    Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2020
    Lipoti la caka ca utumiki ca 2020 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2019
    Lipoti la caka ca utumiki ca 2019 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziŵelengelo Zonse za mu 2023
    Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
Onaninso Zina
Lipoti la Caka ca Utumiki ca 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
syr21 tsa. 2

Ziŵelengelo Zonse za mu 2021

  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Ciŵelengelo ca Maiko Ocitila Lipoti: 239

  • Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 119,297

  • Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 21,367,603

  • Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 20,746

  • Ofalitsaa Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila: 8,686,980

  • Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,480,147

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2020: 0.7

  • Onse Amene Anabatizikab: 171,393

  • Avaleji ya Apainiyac Mwezi Uliwonse: 1,350,138

  • Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 398,504

  • Maola Onse Amene Tinathela mu Utumiki: 1,423,039,931

  • Avaleji ya Maphunzilo a Baibod Mwezi Uliwonse: 5,908,167

M’caka ca utumiki ca 2021,e Mboni za Yehova zinaseŵenzetsa ndalama zoposa madola 229 miliyoni posamalila apainiya apadela, amishonale komanso oyang’anila madela pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale na alongo okwana 20,595, amene akutumikila m’maofesi a nthambi. Onse amenewa ali m’Gulu la Padziko Lonse la Atumiki Apadela a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengeloci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.

b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.

c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?”

e Caka ca utumiki ca 2021 cinayamba pa September 1, 2020, ndipo cinasila pa August 31, 2021.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani