Ziwelengelo Zonse za mu 2024
Nthambi za Mboni za Yehova: 84
Maiko Amene Anacitila Lipoti: 240
Mipingo Yonse: 118,767
Amene Anapezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 21,119,442
Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 23,212
Ofalitsa Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikilaa: 9,043,460
Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali Kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,828,124
Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2023: 2.4
Onse Amene Anabatizikab: 296,267
Avaleji ya Apainiyac Mwezi Uliwonse: 1,679,026
Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 867,502
Avaleji ya Maphunzilo a Baibod Mwezi Uliwonse: 7,480,146
Caka ca utumiki ca 2024 cinayamba pa September 1, 2023, ndipo cinatha pa August 31, 2024.
a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyo 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezela ciwelengeloci, onani nkhani ya pa yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?”
b Kuti mudziwe zimene mungacite kuti mubatizike n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” ku Chichewa.
c Mpainiya ndi wa Mboni wobatizika komanso wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.
d Kuti mudziwe zambili, onani nkhani ya pa yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo Lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?” ku Chichewa.