LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsa. 6
  • Yobu Anali ndi Cikhulupililo Cakuti Akufa Adzauka

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yobu Anali ndi Cikhulupililo Cakuti Akufa Adzauka
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mtengo Ukadulidwa Ungaphukenso?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Fanizo la Mtengo wa Maolivi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 March tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 11-15

Yobu Anali ndi Cikhulupililo Cakuti Akufa Adzauka

Yobu anaonetsa kuti anali ndi cikhulupililo cakuti Mulungu adzamuukitsa

14:7-9, 13-15

Citsa ca mtengo wouma wa maolivi ciphukilanso
  • Yobu anaonetsa cikhulupililo cake cakuti Mulungu adzaukitsa akufa pamene anayelekezela ciyembekezoco ndi mtengo, mwina wa maolivi

  • Mtengo wa maolivi akaudula umaphukanso cifukwa cakuti mizu yake imapita pansi kwambili ndiponso imayala malo aakulu. Ngati mizu yake ikali bwino, mtengowu sulephela kuphuka

  • Mvula ikagwa pambuyo pa cilala coopsa, mizu ya citsa couma ca mtengo wa maolivi imaphuka n’kukhala ndi “nthambi ngati mtengo watsopano”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani