LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsa. 6
  • March 28–April 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 28–April 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 March tsa. 6

March 28–April 3

YOBU 11-15

  • Nyimbo 111 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yobu Anali ndi Cidalilo Cakuti Akufa Adzauka”: (Mph. 10)

    • Yobu 14:1, 2—Yobu anafotokoza kutalika kwa moyo wa anthu (w15–CIN 3/1 3; w10 5/1 5 ndime 2; w08–CN 3/1 3 ndime 3)

    • Yobu 14:13-15a—Yobu anadziŵa kuti Yehova sadzamuiŵala (w15–E 8/1 5; w14 1/1 7 ndime 4; w11–CN 3/1 22 ndime 2-4)

    • Yobu 14:15b—Yehova amakonda atumiki ake okhulupilika (w15–E  8/1 7 ndime 3; w14–CN 6/15 14 ndime 12; w11–CN 3/1 22 ndime 3-6)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu (Mph. 8)

    • Yobu 12:12—N’cifukwa ciani Akristu okalamba ndi oyenelela kuthandiza Akristu acinyamata? (g99 8/8 tsa.11, bokosi)

    • Yobu 15:27—Kodi Elifazi anatanthauza ciani pamene anakamba kuti nkhope ya Yobu “yaphimbika ndi mafuta a m’thupi mwake”? (it-1 E 802 ndime 4)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Yobu 14:1-22 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: fg phunzilo 13 ndime 1. Yalani maziko a ulendo wobwelelako. (Mph. 2 kapena zocepelapo)

  • Ulendo Wobwelelako: fg phunzilo 13 ndime 2. Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)

  • Phunzilo la Baibulo: fg phunzilo 13 ndime 3-4 (Mph. 6 kapena zocepelapo)

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 134

  • Zosoŵa za pampingo (Mph. 5)

  • “Ciukililo Cidzatheka Kupitila mu Nsembe ya Dipo”: (Mph. 10) Kukambilana. Ngati n’zotheka tsilizani mwa kuonetsa vidiyo imene inaonetsedwa pa Msonkhano wa Cigawo wa mu 2014 wa mutu wakuti, “Pitilizani Kufunafuna Ufumu wa Mulungu Coyamba.”

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 12 ndime 1-12 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 33 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani