LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • NSANJA YA MLONDA
  • PHUNZITSANI COONADI
  • N’CIFUKWA CIANI MUYENELA KUPHUNZILA BAIBULO? (Vidiyo)
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 November tsa. 1
Alongo alalikila mzimayi m’cinenelo ca citzotzil mu mzinda wa Chiapas ku Mexico

Apainiya alalikila uthenga wabwino m’cinenelo ca citzotzil mu mzinda wa Chiapas ku Mexico

Maulaliki a Citsanzo

NSANJA YA MLONDA

Nsanja ya Mlonda Na. 6 2016 | Masomphenya a Zinthu za Kumwamba

Funso: Munthu atakufunsani kuti kumwamba kuli ciani, mungayankhe bwanji?

Lemba: Yoh. 8:23

Cogaŵila: Nsanja ya Mlonda iyi ikamba zimene Yesu na Atate ŵake atiuza ponena za kumwamba.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: Kodi mau a ulosi awa opezeka m’Baibo agwilizana na zimene zicitika masiku ano?

Lemba: 2 Tim. 3:1-5

Mfundo ya Coonadi: Popeza kuti ulosi wa m’Baibo wokamba za masiku otsiliza ukukwanilitsidwa masiku ano, sitingakayikile kuti nawonso ulosi wokamba za tsogolo labwino udzakwanilitsidwa.

N’CIFUKWA CIANI MUYENELA KUPHUNZILA BAIBULO? (Vidiyo)

N’cifukwa Ciani Muyenela kuphunzila Baibulo? (vidiyo)

Mau oyamba: Titambitsa anthu kavidiyo kamene kakamba za kumene tingapeze mayankho a mafunso ofunika kwambili paumoyo. (Tambitsani mwininyumba kavidiyo kameneka.)

Cogaŵila: Buku ili lifotokoza mmene Mulungu adzathetsela mavuto padziko lapansi malinga n’zimene Baibo imakamba. (Gaŵilani buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa kapena Zimene Baibulo Ingatiphunzitse.)

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani