LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • PHUNZITSANI COONADI
  • N’CIFUKWA CIANI MUYENELA KUPHUNZILA BAIBULO? (Vidiyo)
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 December tsa. 1
Two sisters conduct a Bible study in Chile

Acititsa phunzilo la Baibo ku Chile

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 6 2016 | Kodi Tingapewe Bwanji Matenda?

Funso: Anthu ambili amafuna kukhala na thanzi labwino. Muganiza tingacite ciani kuti tidzichingilize ku matenda?

Lemba: Miy. 22:3

Cogaŵila: Magazini iyi ifotokoza masitepu amene tingatenge kuti tikhale osamala na kupewa matenda.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: Kodi Mulungu ndiye amacititsa kuti tizivutika kapena ni zinthu zina?

Lemba: Yobu 34:10

Mfundo ya Coonadi: Mulungu sindiye amacititsa kuti tizivutika. Amene amabweletsa mavuto ni Mdyelekezi, anthu amene amapanga zosankha zoipa, ndipo nthawi zina cifukwa ca tsoka cabe. Mulungu iye amafuna kutithandiza tikakhala pamavuto. Amasamaladi za ife.

N’CIFUKWA CIANI MUYENELA KUPHUNZILA BAIBULO? (Vidiyo)

N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (vidiyo)

Funso: Muganiza bwanji, kodi Mulungu ndiye alamulila dziko? [Yembekezani ayankhe.] Mwina mungadabwe na zimene Baibo ikamba. Mvelani zili m’kavidiyo aka. [Tambitsani kavidiyo.]

Cogaŵila: Nkhani 11 ya buku iyi ifotokoza cifukwa cake Mulungu walola kuti tizivutika, na zimene afuna kucitapo. [Mugaŵileni buku ya Zimene Baibo Imaphunzitsa, kapena Zimene Baibulo Ingatiphunzitse.]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani