Aitanila anthu kumisonkhano yampingo pa cisumbu ca ku Cook
Maulaliki a Citsanzo
NSANJA YA MLONDA
Funso: Angelo—Kodi Aliko Zoona?
Lemba: Sal. 103:20
Cogaŵila: Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza zimene Baibo imakamba zokhudza angelo na mmene amakhudzila umoyo wathu masiku ano.
PHUNZITSANI COONADI
Funso: Kodi muganiza kuti sayansi imatsutsana na Baibo?
Lemba: Yes. 40:22
Coonadi: Zimene Baibo imakamba pankhani za sayansi n’zoona.
KAPEPA KOITANILA ANTHU KUMISONKHANO YAMPINGO (inv)
Cogaŵila: Tikuitanilani ku nkhani ya Baibo, kuloŵa ni mahala. Idzakhala ku Nyumba ya Ufumu, pa malo athu olambilila. [Mpatseni kapepa ka ciitano, muonetseni nthawi na malo kumene mumasonkhanila pa wikendi, ndipo chulani mutu wa nkhani ya anthu onse.]
Funso: Kodi munayendako ku Nyumba ya Ufumu? [Ngati n’koyenela, atambitseni vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu?]
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: