LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 November tsa. 7
  • Khalanibe Achelu ndi Okangalika Zinthu Zikasintha mu Umoyo Wanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalanibe Achelu ndi Okangalika Zinthu Zikasintha mu Umoyo Wanu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Khalanibe Achelu ndi Okangalika Kuuzimu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Mwana Woloŵelela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Thandizani a m’Banja Lanu Kukumbukila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 November tsa. 7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Khalanibe Achelu ndi Okangalika Zinthu Zikasintha mu Umoyo Wanu

Kusintha n’kosapeweka, maka-maka m’nthawi ino ya masiku otsiliza. (1 Akor. 7:31) Kaya kusinthako tinali kukuyembekezela kapena ayi, kwabwino kapena koipa, kukhoza kusokoneza kulambila kwathu, ndi ubwenzi wathu na Yehova. Nanga n’ciani cingatithandize kukhalabe achelu ndi okangalika pa nthawi ya masinthidwe? Tambani vidiyo yakuti Kukhalabe Olimba Mwauzimu Pamene Mwasamuka, ndiyeno yankhani mafunso aya:

Pamene banja likonzekela zosamuka, yapatula nthawi yocita Kulambila kwa Pabanja
  • Ni malangizo ati amene m’bale wina anapeleka kwa tate uja?

  • Kodi mfundo ya pa Mateyu 7:25 inagwila nchito bwanji pa banja lija?

  • Kodi banja lija linakonzekela bwanji za kusamuka kwawo? Nanga zimenezi zinawathandiza bwanji?

  • N’ciani cinathandiza banja lija kujaila mu mpingo watsopano na gawo lake?

Kusintha kwakukulu kumene kwanikhudza posacedwa:

Ningaseŵenzetse bwanji mfundo za m’vidiyo imeneyi pa umoyo wanga?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani