CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 15-16
Yang’anani kwa Yehova Kuti Akuthandizeni Kupilila na Kukutonthozani
Njila imodzi imene Yehova amatitonthozela na kutithandiza kupilila, ni kupitila m’Mawu ake. Kodi zitsanzo za m’Baibo izi zingakutonthozeni motani, komanso zingakulimbikitseni bwanji?
Nowa
Yosefe
Davide