Agwila nchito mwakhama pa Beteli ya ku Wallkill, ku New York
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi iliko nthawi pamene munthu wina aliyense sadzadwala?
Lemba: Yes. 33:24
Ulalo: Kodi njala pa dziko lapansi idzatha bwanji?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi njala pa dziko lapansi idzatha bwanji?
Lemba: Sal. 72:16
Ulalo: Kodi tili na ciyembekezo canji cokhudza okondedwa athu amene anamwalila?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Kodi tili na ciyembekezo canji cokhudza okondedwa athu amene anamwalila?
Lemba: Yoh. 5:28, 29
Ulalo: N’cifukwa ciani tingakhulupilile kuti zimene Baibo inalonjeza zidzakwanilitsika?