LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 10
  • Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 10

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama

Timaonetsa nzelu na kuzindikila ngati timvela malamulo a Mulungu (Deut. 4:6; it-2 1140 ¶5)

Ambili akaona zocita zathu amazindikila kuti malamulo a Mulungu ni anzelu (Deut. 4:6; w99 11/1 20 ¶6-7)

Anthu a Yehova ali na umoyo wabwino kwambili kuposa anthu ena (Deut. 4:7, 8; w07 8/1 29 ¶13)

Anthu ambili amabwela m’gulu la Yehova akaona makhalidwe abwino a anthu amene amatsatila malamulo a Mulungu na mfundo zake.

M’bale amene acita ulaliki wa kasitandi waona munthu wataya kacikwama ka ndalama, ndipo mayi amene ali pa malo odyela apafupi akuona zimenezo.
M’bale akupatsa munthu kacikwama kake kamene kanam’tayika, ndipo mayi amene ali pa malo odyela akuona zimenezo.

Ni madalitso otani amene mwapeza cifukwa cotsatila malangizo a Yehova anzelu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani