LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 12
  • Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Zimene Makolo Angaphunzile kwa Manowa na Mkazi Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova

Makolo ayenela kukulitsa cikondi cawo pa Yehova (Deut. 6:5; w05 6/15 20 ¶11)

Ayenela kupeleka citsanzo cabwino kwa ana awo (Deut. 6:6; w07 5/15 15-16)

Ayenela kuphunzitsa ana awo za Yehova kaŵili-kaŵili (Deut. 6:7; w05 6/15 21 ¶14)

Kuwonjezela pa kulambila kwa pabanja, ni mipata ina iti imene mungaphunzitsile ana anu kukonda Yehova na mfundo zake?

Tate na mwana wake akupanga kaiti. Kumbuyo kwawo kuli nkhani zokamba za mbalame za mutu wakuti ‘Kodi Zinangochitika Zokha?’
Tate akambilana na mwana wake wamkazi pamene mwanayo apenta cithunzi ca mtengo wa maapozi. Tateyo akuloza maapozi amene ali m’mbale patsogolo pawo.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani