LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 8
  • Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • “Usadzacite Nawo Mgwilizano wa Ukwati”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • “Ine Ndinauka Monga Mai mu Isiraeli”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Akazi Aŵili Olimba Mtima
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 8
Mneneli wamkazi Debora wakhala patsinde pa mtengo wa kanjedza, ndipo akulimbikitsa Baraki kuti athandize anthu a Mulungu.

Debora akulimbikitsa Baraki kuti athandize anthu a Mulungu

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake

Mdani woopsa anali kupondeleza Aisiraeli (Ower. 4:3; 5:6-8; w15 9/1 12-13)

Yehova anautsa Debora kuti athandize anthu ake (Ower. 4:4-7; 5:7; w15 9/1 13 ¶1; onani cithunzi ca pacikuto)

Yehova anagwilitsila nchito Yaeli popha Sisera (Ower. 4:16, 17, 21; w15 9/1 15 ¶1)

Zithunzi: 1. Mneneli wamkazi Debora wakhala patsinde pa mtengo wa kanjedza, ndipo akulimbikitsa Baraki kuti athandize anthu a Mulungu. 2. Yaeli wanyamula cikhomo ca hema na nyundo, ndipo ali pafupi na Sisera amene ali mtulo tofa nato.

Kodi nkhani imeneyi ionetsa kuti Yehova amawaona bwanji akazi?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani