LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 12
  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Akulu Angathandizile Ena Kukhala Oyenelela Maudindo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Asilikali a Yehova Amoto
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 12
Elisa akuona pamene Eliya akugaŵa madzi a mtsinje wa Yorodano poseŵenzetsa covala cake ca uneneli.

Elisa akuona pamene Eliya akucita cozizwitsa

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Mafumu.]

Elisa anaona pamene Eliya anali kucita cozizwitsa (2 Maf. 2:8; w15 4/15 13 ¶15; onani cithunzi ca pacikuto)

Elisa modzicepetsa anagwilitsa nchito zimene Eliya anam’phunzitsa (2 Maf. 2:13, 14; w15 4/15 13 ¶16)

Mkulu akumvetsela m’bale amene akuyeseza nkhani. Mkuluyo ali na kabuku ka “Kuphunzitsa” kotsegula.

Mumpingo, Yehova anapatsa akulu udindo wophunzitsa ena. (2 Tim. 2:2) Pamene akulu akukuphunzitsani, khalani wodzipeleka, wodalilika, komanso wodzicepetsa.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani