LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 10
  • Mukhuthulileni za Mumtima Mwanu Yehova M’pemphelo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mukhuthulileni za Mumtima Mwanu Yehova M’pemphelo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Hana Apemphela Kuti Akhale na Mwana
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Kumvela Kumaposa Nsembe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Lolani Kuti Yehova Akutonthozeni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
  • Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 10
Hana akupemphela kwa Yehova.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mukhuthulileni za Mumtima Mwanu Yehova M’pemphelo

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Samueli.]

Hana anapemphela kwanthawi yaitali kwa Yehova (1 Sam. 1:10, 12, 15; ia 55 ¶12)

Hana anasiya m’manja mwa Yehova mavuto ake (1 Sam. 1:18; w07 3/15 16 ¶4)

Tikam’khuthulila za mumtima mwathu Yehova, tingakhale na cidalilo cakuti adzatipatsa mphamvu na kuticilikiza.—Sal. 55:22; 62:8.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani