CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kumvela Kumaposa Nsembe
Mneneli wa Yehova anapatsa Mfumu Sauli malangizo omveka bwino (1 Sam. 15:3)
Sauli anayesa kudzilungamitsa atalephela kutsatila malangizo onse a Yehova (1 Sam. 15:13-15)
Yehova sakondwela na kulambila kwa anthu amene samumvela (1 Sam. 15:22, 23; w07 6/15 26 ¶4; it-2 521 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimamvela malangizo onse a gulu la Yehova mofulumila?’