LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 12
  • Yembekezelani Yehova Moleza Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yembekezelani Yehova Moleza Mtima
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Khalanibe Odzicepetsa Zinthu Zikakuyendelani Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Yocititsa Cidwi Yoonetsa Kulimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 12
Davide na mmodzi wa amuna ake abisala kumbuyo kwambili mkati mwa phanga, pamene Sauli akutuluka. Davide watambasula manja ake poletsa mwamunayo, yemwe wanyamula lupanga, kuti asaphe Sauli.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yembekezelani Yehova Moleza Mtima

Davide anali na mwayi wothetsa vuto lake (1 Sam. 24:3-5)

Davide anaona vuto lake mmene Yehova anali kulionela, ndipo anadziletsa (1 Sam. 24:6, 7)

Davide anali na cikhulupililo cakuti Yehova adzathetsa vuto lake (1 Sam. 24:12, 15; w04 4/1 16 ¶8)

Mofanana na Davide, tiyenela kuyembekezela Yehova moleza mtima, m’malo mogwilitsila nchito njila zimene si za m’Malemba pothetsa mavuto athu.—Yak. 1:4; w04 6/1 22-23.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani