LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 2
  • Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kumvela Kumaposa Nsembe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yembekezelani Yehova Moleza Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Khalanibe Odzicepetsa Zinthu Zikakuyendelani Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo

Davide anafuna-funa njila yothaŵila Sauli (1 Sam. 27:5-7; it-1 41)

Davide anateteza malile a dziko la Yuda (1 Sam. 27:8, 9; w21.03 4 ¶8)

Davide sanamuululile zonse Mfumu Akisi (1 Sam. 27:10-12; it-2 245 ¶6)

M’bale wangokhala cete pamene apolisi akum’panikiza na mafunso.

Masiku ano, olamulila angaike ziletso pa nchito yathu ya Ufumu na kutifunsa za abale athu. Pa nthawi ngati zimenezi, n’canzelu kukhala cete kuti tisaike abale athu pa ciopsezo.—Miy. 10:19; 11:12; Mlal. 3:7.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani