LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 8
  • Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Niyenela Kucita Ciani Nikapanga Colakwa?
    Mayankho pa Mafunso 10 Amene Acicepele Amafunsa
  • Tengelani Citsanzo ca Mmene Yehova Amalamulila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kuona Zolakwa Moyenelela
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Asa Anacita Zinthu Molimba Mtima—Kodi Inunso Mumatelo?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 8
Mlongo akuŵelenga Baibo, ndipo akusinkhasinkha zocita za Adoniya. Zithunzi: 1. Adoniya wagwila nyanga ya guwa lansembe. 2. Adoniya akucondelela Bati-seba.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Mafumu.]

Adoniya anacitilidwa cifundo pambuyo pokonza ciwembu cakuti akhale mfumu (1 Maf. 1:5, 52, 53; it-2 987 ¶4)

Adoniya sanaphunzilepo kanthu pa colakwa cake, ndipo analangidwa (1 Maf. 2:15-17, 22, 23; it-1 49)

Munthu wanzelu amaphunzilapo kanthu pa zolakwa zake. Koposa pamenepo, amaphunzilapo kanthu pa zolakwa za ena.—1 Akor. 10:11.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani