LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 14
  • Nyamulani Mwana Wanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Nyamulani Mwana Wanu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Thaŵilani kwa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Pemphelo Linasonkhezela Yehova Kucitapo Kanthu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 14
Mayi wa ku Sunemu mwacimwemwe wakumbatila mwana wake amene wauka kwa akufa ndipo Elisa akuyang’ana.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nyamulani Mwana Wanu

Mayi wa ku Sunemu anam’celeza bwino kwambili Elisa kunyumba kwawo (2 Maf. 4:8-10)

Yehova anadalitsa mayiyo mwa kum’patsa mwana (2 Maf. 4:16, 17; w17.12 4 ¶7)

Yehova anaukitsa mwana wa mayiyo poseŵenzetsa Elisa (2 Maf. 4:32-37; w17.12 5 ¶8)

Kodi muli na cisoni cifukwa munatayikilidwa mwana wanu? Dziŵani kuti Yehova nayenso cimamuwawa. Posacedwapa, iye adzamuukitsa mwana wanu wokondedwa. (Yobu 14:14, 15) Ndithudi, idzakhala nthawi yokondweletsa ngako imeneyo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani