LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 14
  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Nyamulani Mwana Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Tate Apeleka Uphungu Wacikondi kwa Mwana Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 14
Mfumu Davide akuonetsa Solomo anchito amene akukonza zipangizo zomangila kacisi.

Davide akupeleka kwa Solomo anchito komanso zipangizo zoseŵenzetsa pomanga kacis

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thandizani Acinyamata Kuti Apambane

Davide anadziŵa kuti mwa thandizo la Yehova, Solomo adzakwanitsa kuyang’anila nchito yomanga kacisi (1 Mbiri 22:5; w17.01 29 ¶8)

Davide analimbikitsa Solomo kudalila Yehova na kucitapo kanthu (1 Mbiri 22:11-13)

Davide anacita zonse zotheka kuti athandize Solomo (1 Mbiri 22:14-16; w17.01 29 ¶7; onani cithunzi pacikuto)

Zithunzi: 1. Mkulu akuphunzitsa m’bale wacinyamata mosamalila magawo a mpingo. Mkuluyo akuonetsa m’baleyo mapu ya gawo la mpingo, fomu yogaŵila magawo, komanso khadi ya gawo la wofalitsa. 2. M’bale wacinyamatayo akufotokozela m’bale wina moseŵenzetsela khadi ya gawo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningawathandize bwanji acinyamata mumpingo mwathu kupeza cimwemwe komanso cipambano pamene akutumikila Yehova?’—w18.03 11-12 ¶14-15.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani