LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsa. 2
  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Asilikali a Yehova Amoto
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Nyamulani Mwana Wanu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani Yophunzitsa Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 November tsa. 2
Elisa akulongoza mtumiki wake amene ali wodabwa poona mahachi na magaleta ambili ankhondo oyaka moto amene azungulila gulu la asilikali la Asiriya.

Elisa akuuza mtumiki wake kuti: “Ife tili ndi ambili kuposa amene ali ndi iwowo.”​—2 Maf. 6:16

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo

Elisa na mtumiki wake anazungulilidwa na adani (2 Maf. 6:13, 14; it-1 716 ¶4)

Elisa anakhalabe wodekha ndipo analimbikitsa mtumiki wake (2 Maf. 6:15-17; w13 8/15 30 ¶2; onani cithunzi ca pacikuto)

Mozizwitsa, Yehova anapulumutsa Elisa na mtumiki wake (2 Maf. 6:18, 19; it-1 343 ¶1)

Yesu na gulu lake lankhondo lakumwamba akuyang’ana apolisi na asilikali omwe akhamukila mumsewu wa mumzinda. M’bale akuloŵetsa Mboni ziŵili m’nyumba mwake.

Yehova ni wamphamvu kuposa adani athu. Ngati tingayang’ane malo okhala zolengedwa zauzimu na kuona mmene Yehova akutetezela anthu ake, kodi muganiza tingaone ciyani?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani