LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsa. 7
  • Mayi Woipa Komanso Wofunitsitsa Ulamulilo Analangidwa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mayi Woipa Komanso Wofunitsitsa Ulamulilo Analangidwa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • “Nyumba Yonse ya Ahabu Idzafafanizidwa”—2 Maf. 9:8
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehoyada Anali Wolimba Mtima
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli na Malile
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 November tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mayi Woipa Komanso Wofunitsitsa Ulamulilo Analangidwa

Ataliya anapha ana onse acifumu n’colinga cakuti azilamulila Yuda (2 Maf. 11:1; it-1 209; onani chati yakuti “‘Nyumba Yonse ya Ahabu Idzafafanizidwa’—2 Maf. 9:8”)

Yehoseba anabisa Yehoasi, amene anali woloŵa ufumu (2 Maf. 11:2, 3)

Mkulu wa Ansembe Yehoyada anaika Yehoasi kukhala mfumu, ndipo anapha mayi woipa Ataliya, amene mwina ndiye anali wothela m’nyumba ya Ahabu (2 Maf. 11:12-16; it-1 209)

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: Kodi nkhaniyi ionetsa bwanji kuti mawu a pa Miyambo 11:21 komanso pa Mlaliki 8:12, 13 ni oona?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani