LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 2
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Odzicepetsa?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Odzicepetsa?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Yosiya Anali ndi Anzake Abwino
    Phunzitsani Ana Anu
  • Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa “Uta”?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yosiya Anali Kukonda Cilamulo ca Mulungu
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Khalanibe Maso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 2
Mfumu Yosiya akumvetsela modzicepetsa zimene kalembela wake, Safani, akuŵelenga mu mpukutu.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Odzicepetsa?

Yosiya anali wofunitsitsa kukondweletsa Yehova (2 Maf. 22:1-5)

Iye modzicepetsa anavomeleza zolakwa za anthu ake (2 Maf. 22:13; w00 9/15 29-30)

Cifukwa cakuti Yosiya anali wodzicepetsa, Yehova anam’dalitsa (2 Maf. 22:18-20; w00 9/15 30 ¶2)

Yehova amatiyanja ngati modzicepetsa tipempha citsogozo cake, kuvomeleza zolakwa zathu, na kukonza njila zathu.—Yak. 4:6.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani