LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 12
  • Kutsatila Malangizo Kumacititsa Kuti Zinthu Zitiyendele Bwino

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kutsatila Malangizo Kumacititsa Kuti Zinthu Zitiyendele Bwino
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tate Apeleka Uphungu Wacikondi kwa Mwana Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • ‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Khalanibe Acimwemwe Ngakhale Pamene Mwakumana na Zolefula
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 12
Mfumu Davide akuimba na kuvina pamodzi na Aisiraeli ena, pamene Alevi anyamula likasa la pangano.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kutsatila Malangizo Kumacititsa Kuti Zinthu Zitiyendele Bwino

Davide anakonza zokatenga likasa la pangano kuti alibweletse ku Yerusalemu (1 Mbiri 13:3)

Zinthu sizinamuyendele bwino pamene iye analola kuti likasalo linyamulidwe mosayenela (1 Mbiri 15:13; w03 5/1 10-11)

Pambuyo pofufuza malangizo a Yehova, zinthu zinamuyendela bwino Davide (1 Mbiri 15:2; 16:11; w03 5/1 11 ¶13)

Yehova amayamikila zolinga zathu zabwino. Komabe, kuti zocita zathu zimukondweletse, tiyenela kutsatila malangizo ake.—Deut. 30:16.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani