LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 12
  • Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mudzapeleka Nsembe Kaamba Ka Ufumu?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni.”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Anthu Okhulupilika Amasunga Malonjezo Awo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova

Mabanja ena anapemphedwa kusiya nyumba na minda yawo kuti akakhale mumzinda wa Yerusalemu (Neh. 11:1; w98 10/15 22 ¶13)

Amene anadzipeleka kucita zimenezi anadalitsidwa (Neh. 11:2; w86 2/15 26)

Madalitso a Yehova nthawi zonse amakhala oculuka kuposa zilizonse zimene tingadzimane (Malaki 3:10; w16.04 7 ¶15)

Zithunzi: 1. Mwamuna na mkazi wake akulongedza katundu wawo m’cola na m’mabokosi. 2. Banja limodzimodzilo tsopano likutumikila ku dziko lina, ndipo likulalikila uthenga wabwino kwa mzimayi.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ni madalitso otani amene napeza cifukwa codzimana kuti nitumikile Yehova?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani