LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 2
  • Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Thandizani Acinyamata Kuti Apambane
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Esitere Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 2
Esitere wakhala payekha osati pa gulu la atsikana ena. Iye akuyang’ana mbalame zimene zikumwa madzi padziŵe la panyumba pamene atsikana enawo akutangwanika na kudzikongoletsa. Mlonda akuwayang’anila.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere

[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Esitere.]

Esitere anali mkazi wokongola kwambili (Esitere 2:7)

Esitere anakhalabe wodzicepetsa ngakhale pamene ena anamuyamikila na kumutamanda mopambanitsa (Esitere 2:​9, 15; w17.01 25 ¶11; ia 130 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zokamba na zocita zanga zimaonetsa kuti ndine wodzicepetsa?’—w17.01 25 ¶12.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani