LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 7
  • Mukhale Okhutila Ndi Zimene Muli Nazo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mukhale Okhutila Ndi Zimene Muli Nazo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Lekani Kuda Nkhawa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Kodi Ndalama N’zimene Zimabweletsa Mavuto Onse?
    Kuyankha Mafunso Okhudza Baibo
  • Kodi Baibo Imakamba Ciyani pa Zanchito Komanso Ndalama?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Kodi ‘Munaphunzila Cinsinsi’ Cokhala Wokhutila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Mukhale Okhutila Ndi Zimene Muli Nazo”

Ngati tilibe zinthu zambili zakuthupi, tingayesedwe kuti ticite zinthu zimene zingaononge ubale wathu na Yehova. Mwacitsanzo, tingalandile mwayi wa nchito ya ndalama zambili, koma imene ingamatidyele nthawi yocita zinthu zauzimu. Kusinkhasinkha lemba la Aheberi 13:5 kungatithandize.

“Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama”

  • Mwa pemphelo, santhulani kaonedwe kanu ka ndalama, ndiponso ganizilani citsanzo cimene mukupeleka kwa ana anu.—g 9/15 6.

“Mukhale okhutila ndi zimene muli nazo pa nthawiyo”

  • Unikaninso bwino mmene mumaonela zinthu zofunika kwambili pa umoyo.—w16.07 7 ¶1-2.

“Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono”

  • Dalilani Yehova kuti adzakuthandizani kupeza zofunikila pa umoyo ngati mupitiliza kuika Ufumu patsogolo.—w14 4/15 21 ¶17.

Zithunzi: Tumapikica twa muvidiyo yakuti “Mmene Abale Akukhalilabe pa Mtendele Olo Kuti Akukumana na Mavuto a Zacuma.” 1. Miguel akukanya fulawo pafupi na uvuni yapanja. 2. Akuchisa zovala. 3. Akudziyang’ana pagalasi uku akumwetulila pamene akukonzekela kukagwila nchito ku sitolo yogulitsa zitsulo.

TAMBANI VIDIYO YAKUTI MMENE ABALE AKUKHALILABE PA MTENDELE OLO KUTI AKUKUMANA NA MAVUTO A ZACUMA, KENAKO YANKHANI FUNSO ILI:

Kodi mwaphunzilapo ciyani pa citsanzo ca m’bale Miguel Novoa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani