LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 5
  • Lekani Kuda Nkhawa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Lekani Kuda Nkhawa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Mukhale Okhutila Ndi Zimene Muli Nazo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mungamutumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pitilizani Kuonetsa Cikondi Cosasintha
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 5

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Lekani Kuda Nkhawa

Mbalame; Maluŵa

Pa Ulaliki wake wa pa Phili, Yesu anati: “Lekani kudela nkhawa moyo wanu.” (Mat. 6:25) Ngakhale kuti n’kwacibadwa anthu opanda ungwilo okhala m’dziko la Satana kukhala na nkhawa nthawi zina, Yesu anaphunzitsa otsatila ake kuti afunika kupewa kuda nkhawa monyanya. (Sal. 13:2) Cifukwa ciani? Cifukwa kukhala na nkhawa kwambili, ngakhale pa zofunika za tsiku na tsiku, kungaticenjeke na kutilepheletsa kufuna Ufumu coyamba. (Mat. 6:33) Mfundo zina zimene Yesu anakamba zingatithandize kupewa nkhawa zosafunikila.

  • Mat. 6:26—Tingaphunzile ciani mwa kuona zimene mbalame zimacita? (w16.07 mape. 9-10 mapala. 11-13)

  • Mat. 6:27—N’cifukwa ciani kukhala na nkhawa zosayenelela n’kotayitsa cabe nthawi? (w05 11/1 peji 22 pala. 5)

  • Mat. 6:28-30—Tingaphunzilepo ciani pa maluŵa akuchile? (w16.07 mape. 10-11 mapa. 15-16)

  • Mat. 6:31, 32—Kodi Akhristu amasiyana bwanji ndi anthu ena? (w16.07 peji 11 pala. 17)

Ni zinthu ziti zimene nifuna nileke kuda nazo nkhawa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani