MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA | ANTHU OKWATILANA
Zimene Mungacite Kuti Banja Likhale Lacimwemwe: Muzicita Zinthu Monga Timu
Vidiyoyi ionetsa zimene anthu okwatilana angacite kuti azicita zinthu mogwilizana monga timu, n’colinga coti azisangalala m’banja lao.