May 1 Zamkati NKHANI YA PACIKUTO | KODI NDANI AMADZIŴADI ZAMTSOGOLO? Zimene ena amalosela zimacitika, koma zambili sizimacitika NKHANI YA PACIKUTO Kodi Ndani Amadziŵadi Zamtsogolo? Mmene ‘Tingayankhile Munthu Wina Aliyense’ Muzionetsa Khalidwe Lopambana mu Ulaliki Yehova ndi Mulungu Wadongosolo Kodi Mumayendela Limodzi ndi Gulu la Yehova? KUCEZA NDI MNZATHU Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Yesu? Kodi Mudziŵa? Kuyankha Mafunso a m’Baibulo