- 
	                        
            
            Deuteronomo 12:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        5 Mʼmalomwake, mudzafunefune Yehova Mulungu wanu pamalo alionse amene adzasankhe kuti aikepo dzina lake komanso malo amene azidzakhala pakati pa mafuko anu onse, ndipo muzidzapita kumeneko.+ 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            1 Mafumu 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        16 Kenako mahule awiri anapita kwa mfumu nʼkuima patsogolo pa mfumuyo. 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Salimo 122:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        2 Ndipo tsopano mapazi athu aima Pamageti ako iwe Yerusalemu.+ 
 
-