-
2 Mbiri 12:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma iwo akhala atumiki ake kuti adziwe kusiyana kotumikira ine ndi kutumikira mafumu* a mayiko ena.”
9 Choncho Sisaki mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu. Iye anatenga chuma chamʼnyumba ya Yehova+ ndi chuma chamʼnyumba ya mfumu. Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+
-
-
Yeremiya 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiye akadzafunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova Mulungu wathu watichitira zinthu zonsezi?’ udzawayankhe kuti, ‘Mofanana ndi mmene munandisiyira nʼkukatumikira mulungu wachilendo mʼdziko lanu, mudzatumikiranso alendo mʼdziko limene si lanu.’”+
-