Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Samueli 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mlandu umenewu ubwerere pamutu pa Yowabu+ ndi anthu onse a nyumba ya bambo ake. Mʼnyumba ya Yowabu musadzasowe mwamuna wa nthenda yakukha kumaliseche,+ wakhate,+ wogwira ntchito yowomba nsalu,* wophedwa ndi lupanga kapena wosowa chakudya!”+

  • 1 Mafumu 2:31-34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mfumuyo inamuuza kuti: “Chita zimene wakuuzazo. Ukamuphe nʼkumuika mʼmanda ndipo undichotsere ineyo komanso nyumba ya bambo anga magazi amene Yowabu anakhetsa popanda chifukwa.+ 32 Yehova adzachititsa kuti magazi ake akhale pamutu pake, chifukwa anapha ndi lupanga anthu awiri olungama komanso abwino kuposa iyeyo. Anachita zimenezi Davide bambo anga osadziwa. Iye anapha Abineri+ mwana wa Nera mkulu wa asilikali a Isiraeli+ ndiponso Amasa+ mwana wa Yeteri mkulu wa asilikali a Yuda.+ 33 Magazi awo adzakhala pamutu pa Yowabu ndi pamutu pa mbadwa zake mpaka kalekale.+ Koma mtendere wochokera kwa Yehova ukhale kwa Davide, mbadwa zake, nyumba yake ndiponso mpando wake wachifumu mpaka kalekale.” 34 Kenako Benaya mwana wa Yehoyada anapita kuchihemako nʼkukapha Yowabu ndipo anaikidwa mʼmanda kunyumba kwake mʼchipululu.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani