Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 33:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+

  • 2 Mbiri 33:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pambuyo pa zimenezi, Manase anamanga mpanda kunja kwa Mzinda wa Davide,+ kumadzulo kwa Gihoni,+ kuyambira mʼchigwa kukafika ku Geti la Nsomba.+ Mpandawo unazungulira nʼkukafika ku Ofeli+ ndipo anaukweza kwambiri. Iye anaikanso akuluakulu a asilikali mʼmizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.

  • Nehemiya 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani