Salimo 126:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+ Yeremiya 51:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova. Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+
48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova.