-
Yesaya 10:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yehova akadzamaliza ntchito yake yonse mʼphiri la Ziyoni komanso mu Yerusalemu, adzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha mwano umene uli mumtima mwake ndiponso chifukwa chakuti amayangʼana monyada ndi modzikuza.+
-
-
Nahumu 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti,
‘Nineve wawonongedwa!
Ndani adzamumvere chisoni?’
Kodi anthu oti akutonthoze ndidzawapeza kuti?
-