2 “Yehova wandiuza kuti, ‘Upange zomangira komanso magoli ndipo uzivale mʼkhosi mwako. 3 Kenako uzitumize kwa mfumu ya Edomu,+ mfumu ya Mowabu,+ mfumu ya Aamoni,+ mfumu ya Turo+ ndi mfumu ya Sidoni.+ Upatsire amithenga amene abwera ku Yerusalemu kudzaonana ndi Zedekiya mfumu ya Yuda.