2 Mafumu 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mfumu ya Babulo inatenga Mataniya, bambo ake aangʼono a Yehoyakini,+ nʼkuwaika kukhala mfumu mʼmalo mwake. Kenako inawasintha dzina kuti akhale Zedekiya.+ 1 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu. Yeremiya 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya inayamba kulamulira mʼmalo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu chifukwa Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inamuika kuti akhale mfumu mʼdziko la Yuda.+
17 Mfumu ya Babulo inatenga Mataniya, bambo ake aangʼono a Yehoyakini,+ nʼkuwaika kukhala mfumu mʼmalo mwake. Kenako inawasintha dzina kuti akhale Zedekiya.+
15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu.
37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya inayamba kulamulira mʼmalo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu chifukwa Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inamuika kuti akhale mfumu mʼdziko la Yuda.+