Banja la Yehova Logwirizana
M’mawa
- 9:30 Kumvetsera Nyimbo 
- 9:40 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero 
- 9:50 Muziyamikira Mwayi Wanu Wokhala M’banja la Yehova 
- 10:05 Nkhani Yosiyirana: Anathandiza Kuti Ena Azimva Bwino - • Elihu 
- • Lidiya 
- • Yesu 
 
- 11:05 Nyimbo Na. 100 ndi Zilengezo 
- 11:15 Pitirizani Kuthandiza Ena Kuti Akhale M’banja la Yehova 
- 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa 
- 12:00 Nyimbo Na. 135 
Masana
- 1:10 Kumvetsera Nyimbo 
- 1:20 Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero 
- 1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Panyumba Panu Ndi Malo a Mpumulo Ndi Mtendere? 
- 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda 
- 2:30 Nyimbo Na. 136 ndi Zilengezo 
- 2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzilimbikitsa Mtendere - • Muzilankhula ‘Mawu Olimbikitsa’ 
- • ‘Muziyenda M’chikondi’ 
- • Muzipewa Adani Athu 
 
- 3:40 ‘Tisamaleke Kuyamika Mulungu’ Chifukwa cha Abale ndi Alongo Athu 
- 4:15 Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero