Ekisodo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Koma inu sungani zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Yoswa 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsiku lina Yoswa ali pafupi ndi Yeriko, anakweza maso ake ndipo anaona mwamuna wina+ ataima potero patsogolo pake, ali ndi lupanga m’dzanja lake.+ Pamenepo Yoswa anayandikira munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi uli kumbali yathu kapena kumbali ya adani athu?” Yoswa 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Pamapeto pake, ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene anali kukhala kutsidya lina la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu,+ koma ine ndinawapereka m’manja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu. Chotero ndinawafafaniza kuwachotsa pamaso panu.+
11 “Koma inu sungani zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
13 Tsiku lina Yoswa ali pafupi ndi Yeriko, anakweza maso ake ndipo anaona mwamuna wina+ ataima potero patsogolo pake, ali ndi lupanga m’dzanja lake.+ Pamenepo Yoswa anayandikira munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi uli kumbali yathu kapena kumbali ya adani athu?”
8 “‘Pamapeto pake, ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene anali kukhala kutsidya lina la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu,+ koma ine ndinawapereka m’manja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu. Chotero ndinawafafaniza kuwachotsa pamaso panu.+