Ekisodo 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mose anakhalabe m’phirimo ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Mawu Khumi,* pamiyala yosemayo.+ Deuteronomo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditakwera m’phiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita nanu,+ ndinakhala m’phirimo masiku 40, usana ndi usiku,+ (sindinadye mkate kapena kumwa madzi,) 1 Mafumu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+ Mateyu 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atasala kudya masiku 40 usana ndi usiku,+ anamva njala.
28 Choncho Mose anakhalabe m’phirimo ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Mawu Khumi,* pamiyala yosemayo.+
9 Nditakwera m’phiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita nanu,+ ndinakhala m’phirimo masiku 40, usana ndi usiku,+ (sindinadye mkate kapena kumwa madzi,)
8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+