Ekisodo 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anaika zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe m’mphepete mwa nsalu imodzi yakumapeto mwa nsalu zolumikizanazo. Anachitanso chimodzimodzi m’mphepete mwa nsalu yakumapeto kwenikweni, polumikizirana nsalu ziwirizi.+
11 Kenako anaika zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe m’mphepete mwa nsalu imodzi yakumapeto mwa nsalu zolumikizanazo. Anachitanso chimodzimodzi m’mphepete mwa nsalu yakumapeto kwenikweni, polumikizirana nsalu ziwirizi.+