Ekisodo 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo uike zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe kumapeto kwa nsalu imodzi mwa nsalu zolumikizanazo. Uchitenso chimodzimodzi kumapeto kwa nsalu yakumapeto kwenikweni, polumikizirana nsalu ziwirizi.+
4 Ndipo uike zingwe zopota zabuluu zokolekamo ngowe kumapeto kwa nsalu imodzi mwa nsalu zolumikizanazo. Uchitenso chimodzimodzi kumapeto kwa nsalu yakumapeto kwenikweni, polumikizirana nsalu ziwirizi.+