Ekisodo 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma kumbali yakumadzulo, mpanda wa nsaluwo unali mikono 50 kutalika kwake. Kunali nsanamira 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo nsanamirazo.+ Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.
12 Koma kumbali yakumadzulo, mpanda wa nsaluwo unali mikono 50 kutalika kwake. Kunali nsanamira 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo nsanamirazo.+ Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.