Ekisodo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’lifupi mwa bwalolo, kumbali ya kumadzulo, mpanda wa nsaluwo ukhale mikono 50 kutalika kwake, ndipo kukhale nsanamira 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo nsanamirazo.+
12 M’lifupi mwa bwalolo, kumbali ya kumadzulo, mpanda wa nsaluwo ukhale mikono 50 kutalika kwake, ndipo kukhale nsanamira 10 ndi zitsulo 10 zokhazikapo nsanamirazo.+