40 Anabweretsanso nsalu zotchingira+ bwalo, mizati+ ndi zitsulo zokhazikapo mizatiyo,+ nsalu yotchinga+ pachipata cha bwalo, zikhomo za bwalo+ ndi zingwe zogwira mpanda,+ ziwiya zonse+ zogwiritsa ntchito pa utumiki wa pachihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako,