Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+ Ekisodo 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo udzawadzoze ngati mmene wadzozera abambo awo+ kuti atumikire monga ansembe anga. Iwo adzatumikirabe monga ansembe odzozedwa m’mibadwo yawo yonse mpaka kalekale.”+ Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+ 2 Akorinto 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu.
15 Ndipo udzawadzoze ngati mmene wadzozera abambo awo+ kuti atumikire monga ansembe anga. Iwo adzatumikirabe monga ansembe odzozedwa m’mibadwo yawo yonse mpaka kalekale.”+
12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+
21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu.